PAMENE FETEREZA WAVUTA KUPEZA


Maganizo a njira zomwe mungathe kugwiritsa ntchito. Sankhani njira yokugwirani mtima.

1. Kapangidwe ka fetereza wa chilengedwe kapena kuchokera ku zinthu zopeka pafupi

2. Kusintha mbewu zolima

3. Kugwiritsa ntchito mbewu zopilira ku matenda, zocha msanga ndi zopatsa zokolora zambiri

4. Ulimi wa kasakaniza ndi kugwiritsa ntchito manyowa a zinyalala

5. Kubwenzeretsa chonde mu nthaka

6. Kugwiritsa ntchito mathiridwe a fetereza a makono

Design a site like this with WordPress.com
Get started