Malembetsedwe

Lembetsani ngati munthu wamba kuti muthe kugulitsa ndi kugula zinthu kapena kufufuza mayankho. Lembetsani ngati “ofuna kuchita kalondolondo” oyimira ufumu, gulu/komiti kapena bizinesi kuti muthe kulumikizana ndi magulu othandizira ntchito zanu. Lembetsani ngati “ofuna kungosuzumila” ngati mukufuna kungodziwa zambiri.

Mukalembetsa, sankhani “kupitiliza”.

Ndikufuna kulembetsa ngati…

Create your own website, free on WordPress.com.Create your own website.
Start free