Kawiri kawiri timawona ngati chimanga nde yankho la chakudya chopatsa mphamvu komanso chopatsa nthanzi. Koma pali zakudya zina zomwe zimagwira ntchito yomweyo zomwenso zimatheka kulimidwa nthawi ina iliyonse komanso popanda fetereza.
Mukamaliza kuwonera kapena kumvera, kumbukirani kufotokoza m’mene mwakhutitsidwira. DZIWANI ZAMBIRI M’MUSIMU!
Kulima zakudya ndi kubwenzeretsa chilengedwe m’malo okwera (7:27)
Anthu 0 awonera kale. Anthu 0 akuti apezamo zomwe amafuna. Anthu ena akuti adziwa kuti…
Kulima mpendadzuwa mosakaniza ndi soya (14:40)
Anthu 0 awonera kale. Anthu 0 akuti apezamo zomwe amafuna. Anthu ena akuti adziwa kuti…
Kalondolondo (kalembera)
Timachita kalondolondo (kalembera) kuti tithe kukupatsirani zomwe mukufunikira komanso tithandize akonzi ake kukupatsani upangiri ofunikira ndi omveka bwino. Kumbukirani kuti kalondolondo wathu ndi wa chinsisi ndi otetezeka kwa akambelembele, chipongwe ndi chitonzo cha mtundu wina uliwonse. Lowani apa kuti mudziwe m’mene kalembera wathu kuphatikiza zithunzi ndi kanema yemwe timajambula amagwiritsidwira ntchito. Lembetsani apa ngati mwavomereza kutenga nawo gawo mu kalondolondo.