Kugulitsa zokolora zokudya

Yankhani mafunso ali m’musimu kuti muthandizidwe kupeza zogulitsa kapena zochita zina kupatula chimanga chokudya

Mafunso

Funso 1

Ngati kuli kotheka, mungathe kufotokoza chifukwa chake mwaganizira zogulitsa chimanga?

Funso 2

Munakolora chimanga chochuluka bwanji? (chonde, dziwani kuti agent azayenera kuti azatsimikize), nanga mukuganiza kuti chikhonza kukufikitsani mwezi uti (ngakhale osachotsapo)?

Funso 3

A. Ndi mbewu zina ziti zomwe munalima kapena mukulima ngati mulowa m’malo wa chimanga ku mbali ya chakudya chokhutitsa?

B. Mukukonzekera kupeza ndalama munjira zanji zozagulira chimanga, ichi chikatha musanakolore china?

Funso 4

Kupatula chimanga, muli ndi mbewu ina kapena zinthu zina zomwe mungathe kugulitsa koma mumasowa msika wake?

Kodi ena omwe awonera kanemayu akutinji?

Design a site like this with WordPress.com
Get started