ZA ULIMI – UPANGIRI NDI ZIPANGIZO ZA MAKONO

Fufuzani momwe mungathanirane ndi nkhawa zanu. Onani mitu ya zomwe ena afufuza kale. Ngati palibe lembetsani zomwe mukufuna kufufuza.


Jambulitsani Kanema!

Mukhonza kujambulitsa kanema kuti mugawane mzeru ndi anthu ena, muwawunikire kapena akuthandizeni mzeru kuzera pa Tik-tok, Facebook, WhatsApp ndi masamba ena a m’chezo.


Kodi muli ndi mavuto kapena zokhumba ngati izi?

Mapezedwe a fetereza akundivuta/amandivuta


Mbewu/ziweto zanga zagwidwa ndi matenda

Mutha kudziwa dzina ndi zambiri zokhuza matenda ndi njira zothanirana nawo kugwiritsa ntchito zida za makono (ma app), kanema, zojambula ndi zina zotero.

Ndikusowa/ndimasowa njira zopezera ndalama yachangu yogwiritsa ntchito pa khomo tsiku ndi tsiku

Mukhonza kupeza uphungu pa zopinga zomwe mukukumana nazo, ngati mukufuna kudziwa za njira ina kapena ngati mukufufuza njira ina yopezera ndalama.

Sindikupeza/sindimapeza phindu lochuluka kuchokera mu ulimi wanga m’mene ndimakhumbira

Design a site like this with WordPress.com
Get started