Kulembetsa nkhanza kwa a mayi ndi ana osowa pogwira

Chonde, kumbukirani kuti simukuyenera kulembetsa dzina lanu komanso nambara ya foni. Ngati muli kale ndi nambara ya Visitor, itchuleni, kenako pitani pa funso 2, kenako ndikumapitiliza.


1. Nambara yanu ngati Visitor

Choyambirira, awuzeni a agent akuwerengereni nambara yanu ngati Visitor ndipo akupatseni ka pepara kolembadwa nambarayo.

2. Inu ndi amene mwachitiridwa nkhanza kapena pali munthu wina?

~ Ochitiridwa
~ Pali munthu wina

3. Fotokozani nkhani yake

Fotokozani zomwe zinachitika kapena zakhala zikuchitika

Chonde, mubwerenso pakatha ma hora 24 (tsiku limodzi) kapena musiye njira yomwe agent angathe

Design a site like this with WordPress.com
Get started