COMP@SS 2025 (Chichewa)

TAKULANDIRANI PA TSAMBA LOGWIRITSIRA NTCHITO INTERNET M’MIDZI KUDZERA KWA AGENT

Note: DZIWANI KUTI TSAMBALI NDI LA CHIONETSERO CHABE!


Azimayi ndi azibambo, agogo, achinyamata, takulandirani! Khalani omasuka ndi osangalala! Tsopano wina aliyense ochokera m’madera akumidzi akhonza kupeza mwayi ogwiritsa ntchito makina a internet

Iyi ndi njira yomwe mukhonza kugwiritsira ntchito internet mothandizidwa ndi agent pofuna kupeza ndi kufalisa kapena kutumiza uthenga (maphunziro/upangiri, nkhani, misika/malonda) kuti mupeze mayankho a zopinga pa ntchito zanu kapena zochitika zosiyanasiyana za pa khomo ngakhale m’mudzi mwanu, mosavuta.

Takulandirani! Dziwani izi
Takulandirani! Dziwani izi
Design a site like this with WordPress.com
Get started