You have now entered the cyberspace for the rural!
Stories from the digital villages

We’re proud digital villages… We’re now using internet!
Ndife midzi yotsogola yogwiritsa ntchito intaneti!

OmniScope
…where villages can speak up about silenced gender-based violence and child abuse against disadvantaged women and children
…pomwe midzi ikhonza kuwulula za nkhanza kwa a mayi ndi ana osowa pogwira

Umodzi Farms
…where villages are accessing e-agriculture and are monitoring their farming to strengthen their production capacity, sustainability and marketing
…pomwe midzi ikugwiritsa ntchito tekinoloje pofuna kupeza uphungu ndi kuchita kalondolondo wa ulimi wawo pofuna kuzama mu kalimidwe, mu ulimi okhazikika ndi kutsatsa malonda a zokolora

Chikhalidwe eco-centers
…where villages are tracking and collaborating in research and development including promotion of their local conservation initiatives to enhance their effectiveness and eco-tourism as well as other eco-SMEs
…pomwe midzi ikulondoloza, kuchita nawo kafukufuku ndi kupititsa patsogolo ntchito zawo zosamala chilengedwe ndi chikhalidwe komanso kukopa alendo