
Onani zomwe ena agula ndi kugulitsa pa mtengo wa m’tawuni kwanu kwa Muhilili m’musimu!
Kodi muli ndi mafunso kapena zochitika zofunika kulembetsa pa kalondolondo ndi kufalitsidwa? Zokhuza ulimi, kusamala chilengedwe, kukopa alendo, nkhanza, matenda/umoyo, ukhondo, maphunziro, kusaka ntchito kapena njira zophikira ndi kuwunikira?

Chimanga
Lembetsani apa kuti muthe kugulitsa chimanga chanu cha malonda pa mtengo wa m’tawuni kapena kugulitsa mbewu zina kuti musagulitse chimanga chakudya.

Fasa Soya Pieces
Tsopano mukhonza kugula soya pieces wa Fasa pa mtengo wa K300.

Pelekani oda
…ngati palibe zomwe mumafuna. Tsimikizani polembetsa m’musimu. Chonde, dziwani kuti simukuyenera kupeleka ndalama ina iliyonse ngati deposit (dipoziti).

Gulitsani zinthu
Muli ndi malonda ofuna kugulitsa? Lembetsani m’musimu.