Milepa Digital Villages Center

Kodi muli ndi mafunso kapena zochitika zofunika kulembetsa pa kalondolondo ndi kufalitsidwa? Zokhuza ulimi, kusamala chilengedwe, kukopa alendo, nkhanza, matenda/umoyo, ukhondo, maphunziro, kusaka ntchito kapena njira zophikira ndi kuwunikira?

Onani zomwe ena agula ndi kugulitsa pa mtengo wa m’tawuni kwanu ku Milepa m’musimu!

Chimanga

Lembetsani apa kuti muthe kugulitsa chimanga chanu cha malonda pa mtengo wa m’tawuni kapena kugulitsa mbewu zina kuti musagulitse chimanga chakudya.

Matumba a empute (50kg)

Tsopano mukhonza kugula matumba a empute pa mtengo wa K300.

Pelekani Oda

…ngati palibe zomwe mumafuna. Tsimikizani polembetsa m’musimu. Chonde, dziwani kuti simukuyenera kupeleka ndalama ina iliyonse ngati deposit (dipoziti).

Gulitsani zinthu

Muli ndi malonda ofuna kugulitsa? Lembetsani m’musimu.

Design a site like this with WordPress.com
Get started