Masomphenya ndi msanamira zawukadaulo za alimi ena

Zowonera/kanema (Videos)

Mukhonza kuwonera masomphenya ndi msanamira zawukadaulo za alimi ena. Mukhonzanso kujambulitsa kanema wanu kuti ena aphunzire kuchokera kwa inu.

Mukawonera, chonde, tidziwitseni kuti mwakhutitsidwa motani? Mwatolamo chani? Ndi ziti zomwe mukuwona kuti simungakwanitse kapena simunamvatse


Tingakwanitse chani?

M’nyamata wa luntha yemwe anagula zigayo kuchokera mu ulimi wa tomato ndi chiyambi chopanda chithandizo kapena mpamba wawukulu.


Kodi Clement Taonani zimkumuthekera bwanji?


Design a site like this with WordPress.com
Get started