Kutulutsa ndi kugulitsa zokolora za kolite


Za M’musimu

Kanema wasanjidwa motsata malemba (afabeti) kuyambira A mpaka Z. Pali kanema wa mbewu izi ndipo ali mu ndandanda uwu;

A. 1. Anyezi

C. 1. Chimanga

C. 2. Chinangwa

M. 1. Mbatata

M. 2. Mpunga

N. 1. Nkhuku

N. 2. Nthochi

T. 1. Tomato

Anyezi

Kupanga nazare ya anyezi

Kanema uyu akufotokoza m’mene mungakwaniritsire kukhala ndi mbewu ya anyezi ya thanzi komanso yochuluka kuchokera pa nazare

Kutonola ndi kuyanika chimanga

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture


Chinangwa

Kuyeza mulingo wa chinangwa chomwe mungakolore pa munda


Kubzala mbewu yabwino ya chinangwa

Kubzala mbewu yabwino ya chinangwa kumathandiza kukolora zambiri.

Mbatata

Kubzala mbatata (21:00)

Zikupezekera pa tsamba la Gavile_a_Farmer pa YouTube

Mpunga

Kukonza munda wa mpunga

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amakonzera munda wa mpunga kuti azakhale ndi mpunga wa kolite yabwino pokolora

Nazare ya mpunga

Kupanga nazare ya mpunga kumathandiza kukhala ndi zokolora zambiri

Kuwokera mpunga

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amakowokerera mpunga ndi cholinga chofuna kuchulukitsa phindu

Kusunga mbewu ya mpunga

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amasungira mbewu ya mpunga kuti isawonongeke, azathe kukhala ndi zokolora za kolite

Kulima mpunga wa kolite


Kukolora mpunga


Nkhuku

Kuchulukitsa nkhuku za lokolo

Kawirikawiri, nkhuku zalokolo zimaswa anapiye ochepa pazifukwa. Kuti mukhale ndi mazira komanso amapiye ambiri, pali njira zosavuta zomwe mukhonza kutsatira. Pokhala ndi nkhuku zalokolo zambiri komanso zathanzi, mutha kudyetsa banja lanu ndi kupha makwacha. – Access Agriculture

Nthochi

Kupanga mphukira zathanzi za nthochi

Kanema uyu akufotokoza m’mene mungakwaniritsire Kukhala ndi mphukira zathanzi za ntchito zomwe zimathandiza kukhala ndi zokolora zambiri

Tomato

Kusamala Tomato

Kusamala Tomato kuti akhale ndi kolite yokopa ma kasitomala pa msika

Kusunga tomato m’malo ozizilitsira opangidwa kumudzi

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena aku Nigeria amakonzera malo ozizila osungira Tomato ndi cholinga chofuna kuchulukitsa phindu pogulitsa mu nthawi yomwe afuna

Design a site like this with WordPress.com
Get started