Zomvera – Kuweta ziweto zing’onozing’ono

Za M’musimu

Zomverazi zasanjidwa motsata malemba (afabeti) kuyambira A mpaka Z. Pali zomvera za ziweto izi ndipo zili mu ndandanda uwu;

M. 1. Mbuzi

N. 1. Njuchi

N. 2. Nkhuku

Mukamaliza kumvera audio ina iliyonse, adziwitseni alimi amzanu, akonzi ake ndi ena onse m’mene mwakhutitsidwira! 😊

Mbuzi

Ulimi wa mbuzi

Zikupezekera pa app ya Zaulimi. ACE, Welthungerhilfe

Funsani agent kuti akutsekulireni app ya Zaulimi, ku tsamba lomwe kuli zomvera za ulimi wa nkhuku.

Njuchi

Kuweta njuchi

Zikupezekera pa website ya eMlimi. Farm Concern International, World Vision, Africa Farms and Markets

Mverani m’mene mungawetere njuchi kuti mupeze uchi ochuluka komanso wa kolite omwe umatha kuthandiza kupha makwacha

Nkhuku

Ulimi wa nkhuku

Zikupezekera pa app ya Zaulimi. ACE, Welthungerhilfe

Funsani agent kuti akutsekulireni app ya Zaulimi, ku tsamba lomwe kuli zomvera za ulimi wa nkhuku.

Design a site like this with WordPress.com
Get started