Kuweta ziweto zing’onozing’ono


Zomvera


Za M’musimu

Kanemayu wasanjidwa motsata malemba (afabeti) kuyambira A mpaka Z. Pali kanema wa ziweto izi ndipo ali mu ndandanda uwu;

M. 1. Mbira

N. 1. Nkhuku

Mukamaliza kuwonera kanema wina aliyense, adziwitseni alimi amzanu, akonzi ake ndi ena onse m’mene mwakhutitsidwira! 😊


Mbira

Kudyetsa mbira

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amasamalilira ndi kudyetsa mbira kuti zomwe zimathandiza kupha makwacha

Nkhuku

Bizinesi yoweta anapiye a nkhuku pa khomo (10:39)

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture


Kusamala nkhuku za lokolo

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amasamalilira nkhuku za lokolo zomwe zimatha kuthandiza kupeza ndalama yachangu yogwiritsa ntchito pa khomo

Kudyetsa (kuweta) nkhuku za hybrid

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amasamalilira nkhuku za hybrid zomwe zimathandiza kupha makwacha

Design a site like this with WordPress.com
Get started