Kupanga/kuphika zakudya


Za M’musimu

Kanemayu wasanjidwa motsata malemba (afabeti) kuyambira A mpaka Z. Pali kanema wa mbewu ndi ziweto izi ndipo ali mu ndandanda uwu;

C. 1. Chinangwa

M. 1. Mango

M. 2. Mtedza

S. 1. Soya

Mukamaliza kuwonera kanema wina aliyense, adziwitseni alimi amzanu, akonzi ake ndi ena onse m’mene mwakhutitsidwira! ๐Ÿ˜Š


Chinangwa

Kupanga zakudya zokhwasula kuchokera ku chinangwa

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu akuwonetsa m’mene alimi ena amapangira tizakudya tokhwasula kuchokera ku chinangwa kuti azipeza ndalama

Mango

Kufutsa mango

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu mutha Kuphunzira kufutsa mango omwe mukhonza kumagulitsa ngati tokhwasula

Mtedza

Kupanga mafuta kuchokera ku mtedza ndi tokhwasula

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu akuwonetsa m’mene anthu a m’midzi ya ku dziko la Benin amapangira mafuta kuchokera ku mtedza

Soya

Kupanga zokhwasula kuchokera ku soya (8:55)

Zikupezekera pa website ya Access Agriculture

Kanemayu akuwonetsa m’mene mungakwaniritsire kupanga zokhwasula kuchokera ku soya zomwe zikhonza kuthandiza kupeza ndalama yachangu yogwiritsa ntchito pa khomo tsiku ndi tsiku.

Design a site like this with WordPress.com
Get started