Kusintha mbewu Ubwino wa fetereza wa manyowa opangidwa mwa makono kuchokera ku zinyalala Mu kanemayu, alimi a ku Blantyre akufotokoza m’mene anawonera ubwino wa fetereza wa manyowa opangidwa mwa makono kuchokera ku zinyalala. Ubwino wa fetereza opangidwa kuchokera ku mikozo Mu kanemayu, alimi a ku Blantyre akufotokoza m’mene anawonera ubwino wa fetereza opangidwa mwa makono kuchokera ku mikozo. Bwererani pa tsamba loyambirira Dziwani Za interComm