Kapangidwe ka fetereza wa chilengedwe



Zipangizo za makono (ma App)


Zomvera


Zowerenga ndi Zojambula


Zowonera

Mitu

Kanema wasanjidwa motsata malemba (afabeti) kuyambira A mpaka Z, m’malingana ndi zipangizo zopangira feterezayo motere;

1. Biochar

2. Mikozo

3. Tizilombo

4. Zinyalala

Mukamaliza kuwonera kanema wina aliyense, adziwitseni alimi amzanu, akonzi ake ndi ena onse m’mene makhutitsidwira m’malingana ndi zomwe mumafuna kudziwa! 😊

Onani m’musi mwa kanema kuti mudziwe zomwe ena atola mu kanemayo.


Kupanga fetereza wa Biochar

Zikupezekera pa website ya Nthawi Farms


Kupanga fetereza wa Biochar 2

Zikupezekera pa website ya Nthawi Farms


Kupanga fetereza kuchokera ku mikozo (09:17)

Zikupezekera pa Access Agriculture


Kupanga Fetereza Ochokera ku Tizilombo (15:00)

Zikupezekera pa Access Agriculture


Ubwino wa fetereza/kompositi wa manyowa opangidwa mwa makono kuchokera ku zinyalala

Mu kanemayu, alimi a ku Blantyre akufotokoza m’mene anawonera ubwino wa fetereza wa manyowa opangidwa mwa makono kuchokera ku zinyalala.

Zikupezekera pa FarmersPost Umodzi Farms (Facebook) ndi 3rdWorld Village Internet (YouTube)

Anthu ena aphunziramo…


Kupanga Fetereza wa Mbeya (10:45)

Zikupezekera pa Tsamba la Hastings Chiwasa (YouTube)


Kupanga Fetereza wa Mbeya Obeleketsa (11:03)

Zikupezekera pa Tsamba la Gavile_a_Farmer (YouTube)

Design a site like this with WordPress.com
Get started