Kulembetsa mbewu/ziweto zamalonda zofuna kugulitsa pa mtengo wa m’tawuni

Chonde, kumbukirani kuti simukuyenera kulembetsa dzina lanu komanso nambara ya foni. Ngati muli kale ndi nambara ya Visitor, itchuleni, kenako pitani pa funso 2, kenako ndikumapitiliza.


1. Nambara yanu ngati Visitor

Choyambirira, awuzeni a agent akuwerengereni nambara yanu ngati Visitor ndipo akupatseni ka pepara kolembadwa nambarayo.

2. Mulipo gulu kapena nokha?

~ Ndekha
~ Gulu

3. Fotokozani zambiri za mbewu/ziweto zanu za malonda

Tchulani dzina la mbewu/ziweto zomwe mukulima kapena mwakolora, kuchuluka kwake komanso kolite yake ngati kuli kotheka.

Kodi mumafuna kugulitsa pasanathe masiku, masabata kapena miyezi ingati?

Ngati simunakulore, kodi mbewu/ziweto zo zikoloredwa ndi kukhala okonzeka pofika liti?

Chonde, dikirani kwa mphindi 10-15 kapena mubwerenso pakatha ma hora 24 (tsiku limodzi) kapena musiye njira yomwe agent angathe kulumikizana nanu kuti mumve zotsatira ndi kukambirana ndi ogula.

Design a site like this with WordPress.com
Get started