UPHUNGU WA ZAUMOYO

Mutha kupeza malangizo kapena uphungu wa za umoyo mosavuta kuphatikiza matenda, zakulera, ukhondo ndi zina zotero ngati pali zopinga kuti muthe kukafika kuchipatala. Dziwani kuti njirayi si mulowa m’malo wa chipatala kapena ma dokotala.


Online Clinic Yathu

Mutha kupeza malangizo a ku chipatala pa matenda ena ndi ena kudzela pa internet.


Medikal Chat

Mutha kupeza kapena kupeleka uphungu wa za umoyo ndi mankhwala a chilengedwe komanso za ukhondo kugwiritsa ntchito WhatsApp, zithunzi ndi kanema.


All skin diseases and treatment

Mutha kuwona zithunzi za matenda a pa khungu ndi njira zothanirana nawo pamene mukulephera kupita ku chipatala chifukwa cha zopinga zina ndi zina.

Mukalowa apa, pangani download app imeneyi. Ngati munapanga kale, kapena mukamaliza kupanga download, lowani. Ngati pali zomwe musakumvesa, funsani admin akuthandizeni. Fufuzani zithunzi zomwe zikufanana ndi nthenda yanu. Mukapeza, tumizani screenshot kwa admin kuti akuthandizeni kutamthawuzira m’chichewa.


Medgic – AI Skin Analysis

Mutha kudziwa dzina la matenda apakhungu kugwiritsa ntchito app iyi. Jambulani malo agwidwa ndi matendawo ndi kuwunikitsa pa app iyi.

Design a site like this with WordPress.com
Get started