Chonde, kumbukirani kuti simukuyenera kulembetsa dzina lanu komanso nambara ya foni. Ngati muli kale ndi nambara ya Visitor, itchuleni, kenako pitani pa funso 2, kenako ndikumapitiliza.

1. Nambara yanu ngati Visitor
Choyambirira, awuzeni a agent akuwerengereni nambara yanu ngati Visitor ndipo akupatseni ka pepara kolembadwa nambarayo.
2. Mulipo gulu kapena nokha?
~ Ndekha
~ Gulu
3. Fotokozani mbiri yanu
Fotokozani m’mene munayambira kufika pamene muli, zomwe mwakhala mukukwanitsa ndi zopinga zomwe mwakhala mukukumana nazo.
Chonde, mubwerenso pakatha ma hora 24 (tsiku limodzi) kapena musiye njira yomwe agent angathe kulumikizana nanu