Njira kapena masamba omwe mungathe kufufuza ntchito za m’mayiko a kunja kwa dziko la Malawi monga South Africa, United Arab Emirates, Qatar ndi ena onse.

Kuyesera kulumikizana ndi mkulu wa bus company ya T&H
Mukhonza kuyesera kulumikizana ndi mkulu wa bus company ya T&H yemwe wawonetsa chidwi kulemba ntchito m’nyamata wina wa khama yemwe anachitidwa chipongwe ndi anthu ena. Number ya mkuluyi ili pa tsamba lina lotchedwa Mikozi network. Nanu ngati muli a khama, mukhonza kuyesera mwayi kapena kufunsira njira zabwino zopitira ku South Africa kukapeza ntchito.
