
Gulani ndi kugulitsa malonda pa mtengo wa m’tawuni potenga nawo gawo mu kalondolondo/kafukufuku wa ntchito zanu kapena zochitika za pa khomo ngakhale m’mudzi mwanu. Mukhonzanso kupeza upangiri ndi zipangizo za pa internet zothandizira pa ntchito zanu.